1 Mafumu 2:19 BL92

19 Tsono Batiseba ananka kwa mfumu Solomo kukanenera Adoniya kwa iye. Ndipo mfumu inanyamuka kukomana naye, namuweramira nakhalanso pa mpando wace wacifumu, naikitsa mpando wina wa amace wa mfumu, nakhala iye ku dzanja lace lamanja.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 2

Onani 1 Mafumu 2:19 nkhani