20 Pamenepo mkaziyo anati, Ndikupemphani kapempho kamodzi, musandikaniza. Ndipo mfumu inati kwa iye, Tapemphani amai wanga, popeza sindikukanizani.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 2
Onani 1 Mafumu 2:20 nkhani