27 Motero Solomo anacotsa Abyatara asakhalenso wansembe wa Yehova, kuti akakwaniritse mau a Yehova amene aja adalankhula ku Silo za mbumba ya Eli.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 2
Onani 1 Mafumu 2:27 nkhani