28 Ndipo mbiriyi inamfika Yoabu, pakuti Yoabu anapambukira kwa Adoniya, angakhale sanapambukira kwa Abisalomu. Ndipo Yoabu anathawira ku cihema ca Yehova, nagwira nyanga za guwa la nsembe.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 2
Onani 1 Mafumu 2:28 nkhani