1 Mafumu 2:35 BL92

35 Ndipo mfumu inaika Benaya mwana wa Yehoyada m'malo mwace kutsogolera khamu la nkhondo, ndi mfumu inaika Zadoki wansembe m'malo mwa Abyatara.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 2

Onani 1 Mafumu 2:35 nkhani