36 Ndipo mfumu inatuma munthu kukaitana Simeyi, nati kwa iye, Udzimangire nyumba m'Yerusalemu, nukhale komweko osaturukako kumka kwina konse.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 2
Onani 1 Mafumu 2:36 nkhani