23 Ndipo anyamata a mfumu ya Aramu anati kwa iye, Milungu yao nja kumapiri, ndimo m'mene atilakira; koma tikaponyana nao kucidikha, zedi tidzaposa mphamvu.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 20
Onani 1 Mafumu 20:23 nkhani