1 Mafumu 21:19 BL92

19 Ndipo uzilankhula naye, ndi kuti, Atero Yehova, Kodi wapha, mulandanso? Nulankhulenso naye, kuti, Atero Yehova, Paja agaru ananyambita mwazi wa Naboti, pompaja agaru adzanyambita mwazi wako, inde wako.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 21

Onani 1 Mafumu 21:19 nkhani