12 Ndipo aneneri onse ananena momwemo, nati, Kwerani ku Ramoti Gileadi, ndipo mudzacita mwai; popeza Yehova adzaupereka m'dzanja la mfumu.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 22
Onani 1 Mafumu 22:12 nkhani