19 Ndipo anati, Cifukwa cace tamverani mau a Yehova, Ndinaona Yehova alikukhala pa mpando wace wacifumu, ndi khamu lonse la Kumwamba liri ciriri m'mbali mwace, ku dzanja lamanja ndi lamanzere,
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 22
Onani 1 Mafumu 22:19 nkhani