31 Tsono mfumu ya Aramu idalamulira akapitao makumi atatu mphambu ziwiri za magareta ace, niti, Musaponyana ndi anthu ang'ono kapena akuru, koma ndi mfumu ya Israyeli yokha.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 22
Onani 1 Mafumu 22:31 nkhani