32 Ndipo kunali, akapitao a magareta ataona Yehosafati, anati, Zedi uyu ndiye mfumu ya Israyeli imene, napotolokera kukaponyana naye; koma Yehosafati anapfuula.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 22
Onani 1 Mafumu 22:32 nkhani