1 Mafumu 22:38 BL92

38 Ndipo potsuka garetayo pa thawale la ku Samaria agaru ananyambita mwazi wace, pala pamasamba akazi adama, monga mwa mau a Yehova amene ananenawo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 22

Onani 1 Mafumu 22:38 nkhani