1 Mafumu 22:39 BL92

39 Tsono macitidwe ena a Ahabu, ndi zonse adazicita, ndi nyumba ya minyanga adaimanga, ndi midzi yonse adaimanga, kodi sizilembedwa m'buku la macitidwe a mafumu a Israyeli?

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 22

Onani 1 Mafumu 22:39 nkhani