48 Yehosafati anamanga zombo za ku Tarsisi kukatenga golidi ku Ofiri; koma sizinamuka, popeza zinaphwanyika pa Ezioni Geberi.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 22
Onani 1 Mafumu 22:48 nkhani