1 Mafumu 22:50 BL92

50 Ndipo Yehosafati anagona ndi makolo ace, naikidwa ndi makolo ace m'mudzi wa Davide kholo lace; ndipo Yoramu mwana wace anakhala mfumu m'malo mwace.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 22

Onani 1 Mafumu 22:50 nkhani