1 Mafumu 22:51 BL92

51 Ahaziya mwana wa Ahabu anayamba kukhala mfumu ya Israyeli pa Samaria m'caka cakhumi mphambu zisanu ndi ziwiri ca Yehosafati mfumu ya Yuda; nakhala mfumu ya Israyeli zaka ziwiri.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 22

Onani 1 Mafumu 22:51 nkhani