1 Mafumu 3:22 BL92

22 Ndipo mkazi winayo anati, lai, koma wamoyoyu ndi mwana wanga, ndi wakufayu ndi mwana wako. Ndipo uja anati, lai, koma wakufayu ndi mwana wako, ndi wamoyoyu ndi mwana wanga. Motero iwo analankhula pamaso pa mfumu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 3

Onani 1 Mafumu 3:22 nkhani