1 Mafumu 3:23 BL92

23 Tsono mfumu inati, Uyu akuti, Wamoyoyu ndiye mwana wanga ndi wakufayu ndiye mwana wako; ndipo winayo akuti, lai, koma mwana wako ndiye wakufayu, ndi mwana wanga ndiye wamoyoyu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 3

Onani 1 Mafumu 3:23 nkhani