1 Mafumu 3:7 BL92

7 Ndipo tsopano, Yehova Inu Mulungu wanga, mwalonga ine kapolo wanu ufumu m'malo mwa atate wanga Davide, koma ine ndine kamwana, sindidziwa kuturuka kapena kulowa.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 3

Onani 1 Mafumu 3:7 nkhani