1 Mafumu 3:8 BL92

8 Ndipo kapolo wanu ndiri pakati pa anthu anu amene Inu munawasankha, anthu ambirimbiri osawerengeka, kapena kulembeka m'unyinji wao.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 3

Onani 1 Mafumu 3:8 nkhani