1 Mafumu 4:24 BL92

24 Pakuti analamulira dziko lonse liri tsidya lino la Firate, kuyambira ku Tipsa kufikira ku Gaza, inde mafumu onse a ku tsidya tino la Firate; nakhala ndi mtendere kozungulira konseko,

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 4

Onani 1 Mafumu 4:24 nkhani