1 Mafumu 5:3 BL92

3 Mudziwa inu kuti atate wanga Davide sanathe kumangira dzina la Yehova Mulungu wace nyumba, cifukwa ca nkhondo zakumzinga konseko, mpaka atawaika Yehova pansi pa mapazi ace.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 5

Onani 1 Mafumu 5:3 nkhani