1 Mafumu 5:8 BL92

8 Ndipo Hiramu anatumiza kwa Solomo, nati, Ndazimva zija munatumiza kwa inezo, ndidzacita cifuniro canu conse, kunena za mitengo yamkungudza ndi mitengo yamlombwa.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 5

Onani 1 Mafumu 5:8 nkhani