1 Mafumu 6:2 BL92

2 Ndipo nyumbayo mfumu Solomo anaimangira Yehova, m'litali mwace munali mikono makumi asanu ndi limodzi, ndi m'mimba mwace mikono makumi awiri, ndi msinkhu wace mikono makumi atatu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 6

Onani 1 Mafumu 6:2 nkhani