1 Mafumu 6:1 BL92

1 Ndipo kunacitika zitapita zaka mazana anai mphambu makumi asanu ndi atatu ataturuka ana a Israyeli m'dziko la Aigupto, caka cacinai cakukhala Solomo mfumu ya Israyeli, m'mwezi wa Zivi, ndiwo mwezi waciwiri, iye anayamba kumanga nyumba ya Yehova.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 6

Onani 1 Mafumu 6:1 nkhani