1 Mafumu 6:24 BL92

24 Ndipo phiko limodzi la kerubi linali la mikono isanu, ndi phiko lina la kerubi linalinso la mikono isanu; kuyambira ku nsonga ya phiko limodzi kufikira ku nsonga ya phiko lina inali mikono khumi.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 6

Onani 1 Mafumu 6:24 nkhani