1 Mafumu 6:25 BL92

25 Ndi kerubi winayo msinkhu wace unali mikono khumi; akerubi onse awiri anafanana muyeso wao ndi msinkhu wao.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 6

Onani 1 Mafumu 6:25 nkhani