1 Mafumu 7:20 BL92

20 Ndipo panalinso mitu pamwamba pa nsanamira ziwirizo, pafupi pa mimbayo, inali m'mbali mwace mwa ukondewo; ndipo makangazawo anali mazana awiri, akukhala mizere yozinga nda nda mutu winawo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 7

Onani 1 Mafumu 7:20 nkhani