1 Mafumu 7:21 BL92

21 Ndipo anaimiritsa nsanamirazi pa likole la Kacisi; naimiritsa nsanamira ya ku dzanja lamanja, nacha dzina lace Yakini; naimiritsa nsanamira yakumanzere, nacha dzina lace Boazi.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 7

Onani 1 Mafumu 7:21 nkhani