1 Mafumu 7:22 BL92

22 Ndipo pamwamba pa nsanamirazo panali ngati akakombo malembedwe ace; motero anaitsiriza nchito ya nsanamirazo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 7

Onani 1 Mafumu 7:22 nkhani