1 Mafumu 7:25 BL92

25 Linasanjikika pa ng'ombe khumi mphambu ziwiri, zitatu zinapenya kumpoto, zitatu kumadzulo, zitatu kumwera, zitatu kum'mawa; ndipo thawalelo linakhazikika pamwamba pa izo; ndipo nkholo zao zinayang'anana.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 7

Onani 1 Mafumu 7:25 nkhani