26 Ndipo kucindikira kwace kunali ngati m'manja mwa munthu, ndipo mlomo wace unasadamuka ngati mlomo wa comwera, ngati maluwa akakombo, analowamo madzi a mitsuko yaikuru zikwi ziwiri.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 7
Onani 1 Mafumu 7:26 nkhani