1 Mafumu 7:35 BL92

35 Ndipo pamwamba pa phaka panali khoma lozunguniza, msinkhu wace nusu ya mkono; ndi pamwamba pa phaka panali mbano zace ndi matsekerezo a phaka lomwelo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 7

Onani 1 Mafumu 7:35 nkhani