1 Mafumu 7:36 BL92

36 Ndipo m'mapanthi mwa mbano zace ndi pa matsekerezo ace analemba ngati akerubi ndi mikango ndi migwalangwa, monga mwa malo ace a zonsezo, ndi zoyangayanga zozungulira.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 7

Onani 1 Mafumu 7:36 nkhani