1 Mafumu 7:37 BL92

37 Motero anapanga maphaka khumiwo, anafanana mayengedwe ao muyeso wao ndi maonekedwe ao.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 7

Onani 1 Mafumu 7:37 nkhani