23 Yehova Mulungu wa Israyeli, palibe Mulungu wolingana ndi inu m'thambo la kumwamba, kapena pa dziko lapansi, wakusungira cipangano ndi cifundo akapolo anu akuyenda ndi mtima wonse pamaso panu,
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 8
Onani 1 Mafumu 8:23 nkhani