28 Koma muceukire pemphero la kapolo wanu, ndi pembedzero lace, Yehova Mulungu wanga, kumvera kulira ndi kupempha kwace kumene kapolo wanu apempha pamaso panu lero;
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 8
Onani 1 Mafumu 8:28 nkhani