29 kuti maso anu atsegukire nyumba yino usiku ndi usana, kumalo kumene munanenako, Dzina langa lidzakhala komweko; kuti mumvere pemphero limene adzapemphera kapolo wanu lolunjika kumalo kuno.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 8
Onani 1 Mafumu 8:29 nkhani