34 pamenepo mverani Inu m'Mwambamo, ndi kukhululukira cimo la anthu anu Aisrayeli, ndi kuwabwezera ku dziko limene munapatsa makolo ao.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 8
Onani 1 Mafumu 8:34 nkhani