33 Ndipo anthu anu Aisrayeli akawakantha adani ao cifukwa ca kucimwira Inu, ndipo akabweranso kwa Inu, lodi kubvomereza dzina lanu, ndi kupemphera, ndi kupembedza Inu m'nyumba muno;
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 8
Onani 1 Mafumu 8:33 nkhani