1 Mafumu 8:36 BL92

36 pamenepo mverani Inu m'Mwamba, ndi kukhululukira cimo la akapolo anu, ndi la, anthu anu Aisrayeli; pakuti muwaphunzitsa njira yokoma ayenera kuyendamo, ndi kupatsa mvula pa: dziko lanu, limene munawapatsa anthu anu likhale colowa cao.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 8

Onani 1 Mafumu 8:36 nkhani