44 Akaturuka anthu anu kukayambana nkhondo ndi adani ao, kumene konse inu mudzawatuma, ndipo akapemphera kwa Yehova molunjika ku mudzi uno munausankha Inu, ndi ku nyumba ndamangira dzina lanu;
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 8
Onani 1 Mafumu 8:44 nkhani