1 Mafumu 8:43 BL92

43 mverani Inu m'Mwamba mokhala Inu, ndipo citani monga mwa zonse mlendoyo azipempha kwa Inu; kuti anthu onse a dziko lapansi adziwe dzina lanu, kuopa Inu, monga amatero anthu anu Aisrayeli, ndi kuti adziwe kuti nyumba yino ndaimangayi yachedwa dzina lanu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 8

Onani 1 Mafumu 8:43 nkhani