1 Mafumu 8:42 BL92

42 popeza adzamva za dzina lanu lalikuru ndi dzanja lanu lamphamvu ndi mkono wanu wotambasuka; akabwera iyeyo nadzapemphera molunjika ku nyumba yino;

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 8

Onani 1 Mafumu 8:42 nkhani