46 Akacimwira Inu, popeza palibe munthu wosacimwa, ndipo mukakwiya nao ndi kuwapereka kwa adani, kuti iwo awatenge ndende kumka nao ku dziko la adani, ngati kutali kapena kufupi,
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 8
Onani 1 Mafumu 8:46 nkhani