47 ndipo akakumbukila mitima yao, ali kudziko kumene anatengedwa ukapolo, nakalapa, nakapembedza inu m'dziko la iwo anawatenga ndende, ndi kuti, Tacimwa, ndipo tacita mphulupulu, tacita moipa;
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 8
Onani 1 Mafumu 8:47 nkhani