58 kuti atitembenuzire kwa iye yekha mitima yathu iyende m'njira zace zonse, ndi kusunga malamulo ace onse ndi malemba ace ndi maweruzo ace, amene anawalamulira makolo athu.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 8
Onani 1 Mafumu 8:58 nkhani