6 Ndipo ansembe analonga likasa la cipangano ca Yehova kumalo kwace, ku monenera mwa nyumba, ku malo opatulikitsa, munsi mwa mapiko a akerubi,
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 8
Onani 1 Mafumu 8:6 nkhani