5 Ndipo mfumu Solomo ndi msonkhano wonse wa Israyeli wosonkhana kwa iye anali naye kulikasa, naphera nkhosa ndi ng'ombe za nsembe zosawerengeka ndi zosadziwika, cifukwa ca unyinji wao.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 8
Onani 1 Mafumu 8:5 nkhani